2 Samueli 13:5 BL92

5 Ndipo Jonadabu ananena naye, Ugone pa kama wako ndi kudzikokomeza ulikudwala; ndipo pamene atate wako akadzakuona unene naye, Mulole mlongo wanga Tamara abwere kundipatsa kudya, nakonzere cakudyaco pamaso panga kuti ndicione ndi kucidya ca m'manja mwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:5 nkhani