2 Samueli 13:33 BL92

33 Cifukwa cace tsono mfumu mbuye wanga asasauke mtima ndi cinthuci, ndi kuganiza kuti ana amuna onse a mfumu afa; pakuti Amnoni yekha wafa.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:33 nkhani