2 Samueli 13:34 BL92

34 Koma Abisalomu anathawa. Ndipo mnyamata wakudikira anatukula maso ace nayang'ana, ndipo onani, m'mbuyo mwace anthu ambiri analikubwera m'njira yolambalala phiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:34 nkhani