2 Samueli 13:36 BL92

36 Ndipo kunali pakutsiriza iye kulankhula, onani, pomwepo ana amuna a mfumu anafika, nakweza mau ao, nalira misozi; ndi mfumu yomwe ndi anyamata ace analira ndi kulira kwakukuru ndithu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:36 nkhani