2 Samueli 13:37 BL92

37 Koma Abisalomu anathawa, nanka kwa Talimai mwana wa Amihuri mfumu ya ku Gesuri. Ndipo Davide analira mwana wace tsiku ndi tsiku.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 13

Onani 2 Samueli 13:37 nkhani