2 Samueli 14:15 BL92

15 Cifukwa cace tsono cakuti ndadzanena mau awa ndi mbuye wanga mfumu, ndico kuti anthu anandiopsa ine; ndipo mdzakazi wanu ndinati, Ndilankhuletu ndi mfumu; kapena mfumu idzacita copempha mdzakazi wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 14

Onani 2 Samueli 14:15 nkhani