16 Pakuti mfumu idzamvera ndi kupulumutsa mdzakazi wace m'dzanja la munthu wakufuna kundiononga ine pamodzi ndi mwana wanga, kuticotsa ku colowa ca Mulungu.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 14
Onani 2 Samueli 14:16 nkhani