2 Samueli 14:24 BL92

24 Ndipo mfumu inati, Apambukire ku nyumba yaiye yekha, koma asaone nkhope yanga. Comweco Abisalomu anapambukira ku nyumba ya iye yekha, wosaona nkhope ya mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 14

Onani 2 Samueli 14:24 nkhani