2 Samueli 14:31 BL92

31 Pamenepo Yoabu ananyamuka nafika kwa Abisalomu ku nyumba yace, nanena naye, Cifukwa ninji anyamata anu anatentha za m'munda mwanga;

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 14

Onani 2 Samueli 14:31 nkhani