2 Samueli 14:30 BL92

30 Cifukwa cace iye anati kwa anyamata ace, Onani munda wa Yoabu uli pafupi ndi wanga, ndipo iye ali ndi barele pamenepo, mukani mukamtenthere. Ndipo anyamata a Abisalomu anatentha za m'mundawo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 14

Onani 2 Samueli 14:30 nkhani