2 Samueli 15:5 BL92

5 Ndipo kunatero kuti pakusendera munthu ali yense kudzamlambira, iye anatambasula dzanja lace, namgwira, nampsompsona.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:5 nkhani