2 Samueli 15:6 BL92

6 Abisalomu anacitira zotero Aisrayeli onse akudza kwa mfumu kuti aweruze mrandu wao; comweco Abisalomu anakopa mitima ya anthu a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:6 nkhani