2 Samueli 16:6 BL92

6 Ndipo iye anaponya miyala Davide ndi anyamata onse a mfumu Davide, angakhale anthu onse ndi ngwazi zonse zinali kudzanja lamanja ndi ku dzanja lamanzere kwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 16

Onani 2 Samueli 16:6 nkhani