2 Samueli 16:5 BL92

5 Ndipo pakufika mfumu Davide ku Bahurimu, onani, panaturuka pamenepo munthu wa banja la nyumba ya Sauli, dzina lace ndiye Simeyi, mwana wa Gera; iyeyu anaturukako, nayenda natukwana.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 16

Onani 2 Samueli 16:5 nkhani