9 Pomwepo Abisai mwana wa Zeruya ananena ndi mfumu, Garu wakufa uyu atukwaniranji mbuye wanga mfumu? Mundilole ndioloke ndi kudula mutu wace.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 16
Onani 2 Samueli 16:9 nkhani