2 Samueli 17:14 BL92

14 Ndipo Abisalomu ndi anthu onse a Israyeli anati, Uphungu wa Husai M-ariki uposa uphungu wa Ahitofeli. Pakuti kunaikidwa ndi Yehova kutsutsa uphungu wabwino wa Ahitofeli kuti Yehova akamtengere Abisalomucoipa.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 17

Onani 2 Samueli 17:14 nkhani