2 Samueli 17:13 BL92

13 Ndiponso ngati walowa ku mudzi wina, Aisrayeli onse adzabwera ndi zingwe kumudziko, ndipo tidzaukokera kumtsinje, kufikira sikapezeka kamwala kakang'ono kumeneko.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 17

Onani 2 Samueli 17:13 nkhani