2 Samueli 17:12 BL92

12 Comweco tidambvumbulukira pa malo akuti adzapezeka, ndipo tidzamgwera monga mame agwa panthaka, ndipo sitidzasiya ndi mmodzi yense wa iye ndi anthu onse ali naye.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 17

Onani 2 Samueli 17:12 nkhani