11 Koma uphungu wanga ndiwo kuti musonkhanitse Aisrayeli onse kwa inu kuyambira ku Dani kufikira ku Beereseba, monga mcenga uli panyanja kucuruka kwao; ndi kuti muturuke kunkhondo mwini wace.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 17
Onani 2 Samueli 17:11 nkhani