2 Samueli 17:8 BL92

8 Husai anatinso, Mudziwa atate wanu ndi anthu ace kuti ndizo ngwazi, ndipo ali ndi mitima yowawa monga cimbalangondo cocilanda ana ace kuthengo; ndipo atate wanu ali munthu wodziwa nkhondo, sadzagona pamodzi ndi anthu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 17

Onani 2 Samueli 17:8 nkhani