2 Samueli 17:9 BL92

9 Onani, tsopanoli alikubisala kudzenje kapena kwina; ndipo kudzali poyamba kugwa ena, ali yense wakumva adzanena, Alikuphedwa anthu otsata Abisalomu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 17

Onani 2 Samueli 17:9 nkhani