2 Samueli 18:11 BL92

11 Ndipo Yoabu ananena ndi womuuzayo, Ndipo taona, unamuona, tsono unalekeranji kumkantha agwe pansi pomwepo? ndipo ine ndikadakupatsa ndarama khumi ndi lamba.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18

Onani 2 Samueli 18:11 nkhani