17 Ndipo anatenga Abisalomu namponya m'cidzenje cacikuru kunkhalangoko; naunjika pamwamba pace mulu waukuru ndithu wamiyala; ndipo Aisrayeli onse anathawa yense ku hema wace.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18
Onani 2 Samueli 18:17 nkhani