2 Samueli 18:16 BL92

16 Ndipo Yoabu analiza lipenga, ndipo anthu anabwerera naleka kupitikitsa Aisrayeli; pakuti Yoahu analetsa anthuwo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18

Onani 2 Samueli 18:16 nkhani