19 Pomwepo Ahimaazi mwana wa Zadoki anati, Ndithamange nditengere mfumu mau kuti Yehova wabwezera cilango adani ace.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18
Onani 2 Samueli 18:19 nkhani