20 Ndipo Yoabu ananena naye, Sudzakhala iwe wotengera mau lero, koma tsiku lina udzatengera mau; koma lero sudzatengera mau, cifukwa mwana wa mfumu wafa.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18
Onani 2 Samueli 18:20 nkhani