21 Pamenepo Yoabu ananena ndi Mkusi, Kauze mfumu zimene unaziona. Ndipo Mkusi anawerama kwa Yoabu, nathamanga.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18
Onani 2 Samueli 18:21 nkhani