2 Samueli 18:25 BL92

25 Pamenepo mlondayo anapfuula, nauza mfumu. Mfumuyo niti, Ngati ali yekha alikubwera ndi mau. Ndipo iye uja anayenda msanga, nayandikira.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18

Onani 2 Samueli 18:25 nkhani