2 Samueli 18:26 BL92

26 Ndipo mlondayo anaona munthu wina wothamanga; mlonda naitana wakucipata nanena, Taona munthu wina wakuthamanga yekha. Ndipo mfumu inati, iyenso abwera ndi mau.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18

Onani 2 Samueli 18:26 nkhani