2 Samueli 18:27 BL92

27 Mlondayo nati, Ndiyesa kuti kuthamanga kwa wapatsogoloyo kunga kuthamanga kwa Ahimaazi mwana wa Zadoki, Ndipo mfumu inati, iye ndiye munthu wabwino, alikubwera ndi mau okoma.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18

Onani 2 Samueli 18:27 nkhani