2 Samueli 18:28 BL92

28 Ndipo Ahimaazi anapfuula, nanena ndi mfumu, Mtendere. Ndipo anawerama pamaso pa mfumu ndi nkhope yace pansi, nati, Alemekezeke Yehova Mulungu wanu amene anapereka anthu akukwezera dzanja lao pa mbuye wanga mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18

Onani 2 Samueli 18:28 nkhani