2 Samueli 18:31 BL92

31 Ndipo onani, Mkusiyo anafika, nati, Mau akuuza mbuye wanga mfumu; pakuti Yehova anabwezera cilango lero onse akuukira inu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18

Onani 2 Samueli 18:31 nkhani