2 Samueli 18:32 BL92

32 Ndipo mfumu inanena ndi Mkusiyo, Mnyamatayo Abisalomu ali bwino? Mkusiyo nayankha, Adani a mbuye wanga mfumu, ndi onse akuukira inu kukucitirani zoipa, akhale monga mnyamata ujayo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18

Onani 2 Samueli 18:32 nkhani