2 Samueli 18:33 BL92

33 Ndipo mfumuyo inagwidwa cisoni, nikwera ko cipinda cosanja pa cipataco, nilira misozi; niyenda, nitero, Mwana wanga Abisalomu, mwana wanga Abisalomu; mwana wanga! Mwenzi nditakufera ine, Abisalomu, mwana wanga, mwana wanga!

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18

Onani 2 Samueli 18:33 nkhani