2 Samueli 18:5 BL92

5 Ndipo mfumu inalamulira Yoabu nd Abisai ndi ltai, kuti, Cifukwa ca ine mucite mofatsa ndi mnyamatayo, Abisalomu. Ndipo anthu onse anamva pamene mfumu inalamulira atsogoleriwo za Abisalomu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18

Onani 2 Samueli 18:5 nkhani