2 Samueli 19:10 BL92

10 Ndipo Abisalomu amene tinamdzoza mfumu yathu anafa kunkhondo. Cifukwa cace tsono mulekeranji kunena mau akuti abwere nayo mfumuyo?

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:10 nkhani