2 Samueli 19:9 BL92

9 Ndipo anthu onse a m'mafuko onse a Israyeli analikutsutsana, ndi kuti, Mfumuyo inatilanditsa ife m'dzanja la adani athu, natipulumutsa m'dzanja la Afilisti; ndipo tsopano inathawa m'dziko kuthawa Abisalomu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:9 nkhani