2 Samueli 19:8 BL92

8 Pamenepo mfumu inanyamuka, nikakhala pacipata, Ndipo inauza anthu kuti, Onani mfumu irikukhala pacipata; anthu onse nadza pamaso pa mfumu. Koma Aisrayeli adathawa, munthu yense ku hema wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:8 nkhani