2 Samueli 19:12 BL92

12 Inu ndinu abale anga, muli pfupa langa ndi mnofu wanga; cifukwa ninji tsono muli am'mbuyo koposa onse kubwera nayo mfumu?

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:12 nkhani