2 Samueli 19:13 BL92

13 Ndipo munene ndi Amasa, Suli pfupa langa ndi mnofu wanga kodi? Mulungu andilange naonjezepo ngati sudzakhala cikhalire kazembe wa khamu la ankhondo pamaso panga, m'malo mwa Yoabu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:13 nkhani