2 Samueli 19:26 BL92

26 Ndipo anayankha, Mbuye wanga mfumu, mnyamata wanga anandinyenga; pakuti mnyamata wanu ndinati, Ndidzadzimangira buru kuti ndiberekekepo ndi kupita ndi mfumu, pakuti mnyamata wanu ndiri wopunduka.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:26 nkhani