2 Samueli 19:27 BL92

27 Ndipo iye anandinamizira mnyamata wanu kwa mbuye wanga mfumu; koma mbuye wanga mfumu ali ngati mthenga wa Yehova; cifukwa cace citani cimene cikukomerani.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:27 nkhani