2 Samueli 19:29 BL92

29 Ndipo mfumu inanena naye, Ulikulankhulanso bwanji za zinthu zako? Ine ndikuti, Iwe ndi Ziba mugawe dzikolo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:29 nkhani