2 Samueli 19:32 BL92

32 Ndipo Barizilai anali nkhalamba, ndiye wa zaka makumi asanu ndi atatu; ndiye amene anapereka cakudya kwa mfumu muja anagona ku Mahanaimu, pakuti anali munthu womveka ndithu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:32 nkhani