2 Samueli 19:33 BL92

33 Ndipo mfumu inanena ndi Barizilai, Tiyeni muoloke nane, ndipo ndidzakusungani pamodzi ndi ine ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:33 nkhani