2 Samueli 2:11 BL92

11 Ndipo Davide anali mfumu ya nyumba ya Yuda ku Hebroni zaka zisanu ndi ziwiri kudza miyezi isanu ndi umodzi.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2

Onani 2 Samueli 2:11 nkhani