2 Samueli 2:19 BL92

19 Ndipo Asaheli anapitikitsa Abineri. Ndipo m'kuthamanga kwace sanapambukira kulamanja, kapena kulamanzere, pakutsata Abineri.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2

Onani 2 Samueli 2:19 nkhani