2 Samueli 2:21 BL92

21 Ndipo Abineri ananena naye, Patuka iwe kulamanja kapena kulamanzere kwako nudzigwirire wina wa anyamatawo, nutenge zida zace. Koma Asaheli anakana kupambuka pakumtsata iye.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2

Onani 2 Samueli 2:21 nkhani