2 Samueli 2:22 BL92

22 Ndipo Abineri anabwereza kunena kwa Asaheli, Pambuka pakunditsata ine. Ndidzakukanthiranji kukugwetsa pansi? ndikatero ndidzaweramutsanso bwanji nkhope yanga kwa mbale wako Yoabu?

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2

Onani 2 Samueli 2:22 nkhani