32 Ndipo ananyamula Asaheli namuika m'manda a atate wace ali ku Betelehemu. Ndipo Yoabu ndi anthu ace anacezera kuyenda usiku wonse, ndipo kudawacera ku Hebroni.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2
Onani 2 Samueli 2:32 nkhani